Ephesians 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene muŵerenga zimenezi, mungathe kuwona kuti ndikumvetsetsadi chinsinsi chonena za Khristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chimene mukhoza kuzindikira nacho, pakuchiwerenga, chidziwitso changa m'chinsinsi cha Khristu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mukuwerenga izi, inu mudzazindikira za chidziwitso changa pa chinsinsi cha Khristu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cimene mukhoza kuzindikira naco, pakuciwerenga, cidziwitso canga m'cinsinsi ca Kristu,