Ephesians 4:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mau a Mulungu akuti, “Pamene adakwera Kumwamba, adatenga chigulu cha am'ndende, ndipo adagaŵira anthu mphatso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anena, M'mene anakwera kumwamba, anamanga ndende undende, naninkha zaufulu kwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake akunena kuti, “Iye atakwera kumwamba, anatenga chigulu cha a mʼndende ndipo anapereka mphatso kwa anthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anena, M'mene anakwera kumwamba, anamanga ndende undende, Naninkha zaufulu kwa anthu.