Ephesians 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mau akuti “adakwera” tanthauzo lake nchiyani? Ndiye kuti poyamba adaatsikira pansi penipeni pa dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ichi, chakuti, Anakwera, nchiyani nanga koma kuti anatsikiranso ku madera a kunsi kwa dziko?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mawu akuti, “Iye anakwera” akutanthauza chiyani, ngati Iyeyo sanatsikire kunsi kwa dziko lapansi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ici, cakuti, Anakwera, nciani nanga komakuti anatsikiranso ku madera a kunsi kwa dziko?