Ephesians 5:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono popeza kuti ndinu ana okondedwa a Mulungu, muziyesa kumtsanzira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, monga ana okondedwa, tsatirani chitsanzo cha Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa;