Ephesians 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musayanjane nawo anthu ochita zopanda pake za mdima, koma muŵatsutse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo musayanjane nazo ntchito za mdima zosabala kanthu, koma makamakanso muzitsutse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musayanjane nazo ntchito zosapindulitsa za mdima, koma mʼmalo mwake muzitsutse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo musayanjane nazo nchito za mdima zosabala kanthu, koma maka-makanso muzitsutse;