Ephesians 5:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja zimene iwo amachita mobisa, ngakhale kuzitchula komwe kumachititsa manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti zochitidwa nao m'tseri, kungakhale kuzinena kuchititsa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndi zochititsa manyazi ngakhale kutchula zomwe zimachitika mseri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti zocitidwa nao m'tseri, kungakhale kuzinena kucititsa manyazi.