Ephesians 5:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kuŵala kumaunika zinthu, ndipo zonse zimaonekera poyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zinthu zonse potsutsika ndi kuunika, zionekera; pakuti chonse chakuonetsa chili kuunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kuwala kumawunikira zinthu, ndipo chilichonse chimaonekera poyera. Choncho chilichonse choonekera poyera chimasandukanso kuwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zinthu zonse potsutsika ndi kuunika, zionekera; pakuti conse cakuonetsa ciri kuunika.