Ephesians 5:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibiretu munthu amene amadana ndi thupi lake, koma amalidyetsa ndi kulisamala bwino, monga momwe Khristu amachitira Mpingo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti munthu sanadana nalo thupi lake ndi kale lonse; komatu alilera nalisunga, monganso Khristu Mpingo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti palibe amene amadana nalo thupi lake, koma amalidyetsa ndi kulisamalira bwino, monga momwe Khristu amachitira ndi mpingo wake
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti munthu sanadana nalo thupi lace ndi kale lonse; komatu alilera nalisunga, monganso Kristu Eklesia;