Ephesians 6:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Valani zida zonse zimene Mulungu akupatsani, kuti muthe kulimbika polimbana ndi ndale za Satana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tavalani zida zonse za Mulungu, kuti mudzakhoze kuchilimika pokana machenjerero a mdierekezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Valani zida zonse za Mulungu kuti muthe kuyima ndi kukana machenjerero a Satana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tabvalani zida zonse za Mulungu, kuti mudzakhoze kucirimika pokana macenjerero a mdierekezi.