Ephesians 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lonjezolo likuti, “Ukatero, udzakhala wodala, ndipo moyo wako udzakhala wautali pansi pano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti kukhale bwino ndi iwe, ndi kuti ukhale wa nthawi yaikulu padziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ulemekeza abambo ako ndi amayi ako, “zinthu zidzakuyendera bwino ndipo udzasangalala ndi moyo wautali pa dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti kukhale bwino ndi iwe, ndi kuti ukhale wa nthawi yaikuru padziko.