Esther 1:22 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natumiza akalata kumaiko onse a mfumu, kudziko lililonse monga mwa chilembedwe chao, ndi kumtundu uliwonse monga mwa chinenedwe chao, kuti mwamuna aliyense akhale wamkulu m'nyumba yakeyake, nawabukitse monga mwa chinenedwe cha anthu a mtundu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inatumiza makalata ku madera onse a ufumu wake, chigawo chilichonse mʼzilembo zawo ndi ku mtundu uliwonse mʼchiyankhulo chawochawo kulengeza kuti mwamuna ayankhule chilichonse chimene chikumukomera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natumiza akalata ku maiko onse a mfumu, ku dziko liri lonse monga mwa cilembedwe cao, ndi ku mtundu uli wonse monga mwa cinenedwe cao, kuti mwamuna ali yense akhale wamkuru m'nyumba yace yace, nawabukitse monga mwa cinenedwe ca anthu amtundu wace.