Esther 1:7 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nawapatsa chakumwa m'zomwera zagolide, zomwerazo nzosiyanasiyana, ndi vinyo wachifumu anachuluka, monga mwa ufulu wa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapereka zakumwa mʼchikho zagolide zamitundumitundu, ndipo vinyo waufumu anali wochuluka kwambiri monga mwa kukoma mtima kwa mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawapatsa cakumwa m'zomwera zagolidi, zomwerazo nzosiyana-siyana, ndi vinyo wacifumu anacuruka, monga mwa ufulu wa mfumu.