Esther 1:8 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mamwedwewo anali monga mwa lamulo; panalibe kukakamiza; pakuti mfumu idaikira akulu onse a nyumba yake motero, kuti achite monga momwe akhumba aliyense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mwa lamulo la mfumu aliyense anamwa mʼmene anafunira, pakuti mfumu inawuza otumikira ake kuti apatse aliyense monga mwa kukonda kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mamwedwewo anali monga mwa lamulo; panalibe kukakamiza; pakuti mfumu idaikira akulu onse a nyumba yace motero, kuti acite monga momwe akhumba ali yense.