Esther 1:9 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Vasiti yemwe, mkazi wamkulu, anakonzera akazi madyerero m'nyumba yachifumu ya mfumu Ahasuwero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkazi wa mfumu Vasiti nayenso anakonzera phwando amayi ku nyumba ya ufumu ya mfumu Ahasiwero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Vasiti yemwe, mkazi wamkuru, anakonzera akazi madyerero m'nyumba yacifumu ya mfumu Ahaswero.