Esther 10:2 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi zochita zonse za mphamvu yake, ndi nyonga zake, ndi mafotokozedwe a ukulu wa Mordekai, umene mfumu inamkulitsa nao, sizinalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Mediya ndi Persiya?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ntchito zonse zochitika ndi mphamvu zake komanso ndi zonse zofotokoza za ukulu wa Mordekai, kukwezedwa kwake ndi mfumu, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a ku Mediya ndi Peresiya?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi zocita zonse za mphamvu yace, ndi nyonga zace, ndi mafotokozedwe a ukulu wa Moredekai, umene mfumu inamkulitsa nao, sizilembedwa kodi m'buku la mbiri ya mafumu a Mediya ndi Perisiya?