Esther 2:1 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zitatha izi, utaleka mkwiyo wa mfumu Ahasuwero, anakumbukira Vasiti, ndi chochita iye, ndi chomlamulidwira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake mtima wa Ahasiwero utatsika, Ahasiwero anakumbukira Vasiti ndi zimene anachita Vasitiyo. Anakumbukiranso lamulo lomukhudza limene anasindikiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zitatha izi, utaleka mkwiyo wa mfumu Ahaswero, anakumbukila Vasiti, ndi cocita iye, ndi comlamulidwira.