Esther 2:10 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Estere sadawulula mtundu wake ndi chibale chake; pakuti Mordekai adamuuzitsa kuti asadziwulule.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Estere sanawulule mtundu wake ndi abale ake chifukwa Mordekai anamuletsa kutero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Estere sadaulula mtundu wace ndi cibale cace; pakuti Moredekai adamuuzitsa kuti asadziulule.