Esther 2:11 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Mordekai akayendayenda tsiku ndi tsiku kubwalo la nyumba ya akazi, kuti adziwe umo akhalira Estere, ndi chimene chidzamchitikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku ndi tsiku Mordekai ankayendayenda pafupi ndi bwalo la nyumba yosungiramo akazi ija kuti adziwe za moyo wa Estere ndi kuti zinthu zikumuyendera bwanji.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Moredekai akayendayenda tsiku ndi tsiku ku bwalo la nyumba ya akazi, kuti adziwe umo akhalira Estere, ndi cimene cidzamcitikira.