Esther 2:20 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Estere sadawulula chibale chake kapena mtundu wake, monga Mordekai adamuuza; popeza Estere anachita mau a Mordekai monga m'mene analeredwa naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Estere anali asanawululebe za mtundu wake ndi anthu a pa banja lake monga momwe analamulira Mordekai, chifukwa anapitirira kutsata malangizo a Mordekai monga ankachitira pamene ankamulera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Estere sadaulula cibale cace kapena mtundu wace, monga Moredekai adamuuza; popeza Estere anacita mau a Moredekai monga m'mene analeredwa naye.