Esther 2:5 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Panali Myuda m'chinyumba cha ku Susa, dzina lake ndiye Mordekai, mwana wa Yairi, mwana wa Simei, mwana wa Kisi Mbenjamini;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Myuda wina wa fuko la Benjamini, dzina lake Mordekai, mwana wa Yairi, mwana wa Simei, mwana wa Kisi, anali mu mzinda wa Susa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Panali Myuda m'cinyumba ca ku Susani, dzina lace ndiye Moredekai, mwana wa Yairi, mwana wa Simei, mwana wa Kisi Mbenjamini;