Esther 3:14 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a cholembedwacho, ndiwo kuti lichitike lamulo m'maiko onse, analalikidwa kwa anthu onse, kuti akonzekeretu tsiku lomwelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachidule kalatayi inanena kuti mawu olembedwamowo anayenera kuperekedwa ngati lamulo mʼchigawo chilichonse ndi kuti anthu a mtundu uliwonse adziwe ndi kukhala okonzeka pa tsikulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a colembedwaco, ndiwo kuti licitike lamulo m'maiko onse, analalikidwa kwa anthu onse, kuti akonzekeretu tsiku lomwelo.