Esther 3:5 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hamani, pakuona kuti Mordekai sanamweramire kapena kumgwadira, mtima wake unadzala mkwiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hamani ataona kuti Mordekai sankamugwadira kapena kumuweramira, anapsa mtima kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hamani, pakuona kuti Moredekai sanamweramira kapena kumgwadira, mtima wace unadzala mkwiyo.