Esther 3:6 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anachiyesa chopepuka kumthira manja Mordekai yekha; pakuti adamfotokozera mtundu wake wa Mordekai; potero Hamani anafuna kuononga Ayuda onse okhala m'ufumu wonse wa Ahasuwero, ndiwo a mtundu wa Mordekai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hamani atamva kuti Mordekai anali Myuda, anatsimikiza kuti ndi kosakwanira kulanga Mordekai yekha. Mʼmalo mwake anapeza njira yowonongera Ayuda onse okhala mʼdziko lonse limene mfumu Ahasiwero ankalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anaciyesa copepuka kumthira manja Moredekai yekha; pakuti adamfotokozera mtundu wace wa Moredekai; potero Hamani anafuna kuononga Ayuda lonse okhala m'ufumu wonse wa Ahaswero, ndiwo a mtundu wa Moredekai.