Esther 4:13 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Mordekai anawauza ambwezere mau Estere, kuti, Usamayesa m'mtima mwako kuti udzapulumuka m'nyumba ya mfumu koposa Ayuda onse ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Mordekai anawawuza kuti akamuyankhe Estere motere: “Usaganize kuti iwe wekha mwa Ayuda onse udzapulumuka chifukwa chakuti uli mʼnyumba ya mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Moredekai anawauza ambwezere mau Estere, kuti, Usamayesa m'mtima mwako kuti udzapulumuka m'nyumba ya mfumu koposa Ayuda onse ena.