Esther 4:2 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nafika popenyana ndi chipata cha mfumu; popeza sanathe munthu kulowa kuchipata cha mfumu wovala chiguduli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anapita ndi kuyima pa chipata cha mfumu, chifukwa panalibe wina aliyense amaloledwa kulowa pa chipata cha mfumu atavala chiguduli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nafika popenyana ndi cipata ca mfumu; popeza sanathe munthu kulowa ku cipata ca mfumu wobvala ciguduli.