Esther 4:6 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natuluka Hataki kunka kwa Mordekai kukhwalala la mudzi linali popenyana ndi chipata cha mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Hataki anapita kwa Mordekai ku bwalo la mzinda patsogolo pa chipata cha mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naturuka Hataki kumka kwa Moredekai ku khwalala la mudzi linali popenyana ndi cipata ca mfumu.