Esther 5:10 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Hamani anadziletsa, namuka kwao, natumiza munthu kukatenga mabwenzi ake, ndi Zeresi mkazi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
komabe Hamani anadziletsa ndipo anapita ku nyumba kwake. Anayitana abwenzi ake pamodzi ndi mkazi wake Zeresi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Hamani anadziletsa, namuka kwao, natumiza munthu kukatenga mabwenzi ace, ndi Zeresi mkazi wace.