Esther 5:11 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nawawerengera Hamani kulemera kwake kwakukulu, ndi ana ake ochuluka, ndi zonse mfumu idamkuza nazo, ndi umo adamkweza koposa akalonga ndi anyamata a mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hamani anawawuza za kuchuluka kwa chuma chake ndi kuti anali ndi ana aamuna ambiri. Anawawuzanso za mmene mfumu inamukwezera ndi kumuyika kukhala woposa nduna ndi olemekezeka onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawawerengera Hamani kulemera kwace kwakukuru, ndi ana ace ocuruka, ndi zonse mfumu idamkuza nazo, ndi umo adamkweza koposa akalonga ndi anyamata a mfumu.