Esther 5:4 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Estere anati, Chikakomera mfumu, adze mfumu ndi Hamani lero ku madyerero ndinawakonzera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Estere anayankha kuti, “Ngati chingakukomereni, mfumu, mubwere lero pamodzi ndi Hamani kuphwando limene ndakonzera inu mfumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Estere anati, Cikakomera mfumu, adze mfumu ndi Hamani lero ku madyerero ndinawakonzera.