Esther 6:10 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu inati kwa Hamani, Fulumira, tenga chovala ndi kavalo monga umo wanenera, nuchitire chotero Mordekai Myudayo, wokhala pa chipata cha mfumu; kasasowepo kanthu ka zonse wazinena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inalamulira Hamani kuti, “Pita msanga, katenge chovala cha ufumu ndi kavalo ndipo uchite monga wanenera kwa Mordekai Myuda, amene amakhala pa chipata cha mfumu. Usasiyeko china chilichonse chimene wanena.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu inati kwa Hamani, Fulumira, tenga cobvala ndi kavalo monga umo wanenera, nucitire cotero Moredakai Myudayo, wokhala pa cipata ca mfumu; kasasowepo kanthu ka zonse wazinena.