Esther 6:5 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata a mfumu ananena nayo, Taonani, Hamani alikuima pabwalo. Niti mfumu, Alowe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atumiki ake anamuyankha kuti, “Hamani ndiye wayima mu bwalo.” “Mulowetseni,” Mfumu inalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata a mfumu ananena nayo, Taonani, Hamani alikuima pabwalo. Niti mfumu, Alowe.