Esther 6:7 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Hamani kwa mfumu, Munthu amene mfumu ikondwera kumchitira ulemu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Hamani anayankha mfumuyo kuti, “Munthu amene mfumu ifuna kumuchitira ulemu, imuchitire izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Hamani kwa mfumu, Munthu amene mfumu ikondwera kumcitira ulemu,