Esther 7:3 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nayankha mkazi wamkulu Estere, nati, Ngati mwandikomera mtima, mfumu, ndipo chikakomera mfumu, andilekere moyo wanga pa kupempha kwanga, ndi wa anthu a mtundu wanga pa pempho langa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mfumukazi Estere anayankha kuti, “Ngati mwandikomera mtima, inu mfumu, ndipo ngati chingakukomereni mfumu, pempho ndi chokhumba changa ndi ichi, mulole kuti ine ndi abale anga tisungidwe tonse ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nayankha mkazi wamkuru Estere, nati, Ngati mwandikomera mtima, mfumu, ndipo cikakomera mfumu, andilekere moyo wanga pa kupempha kwanga, ndi wa anthu a mtundu wanga pa pempho langa;