Esther 7:4 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti tagulitsidwa; ine ndi anthu a mtundu wanga, kuti ationonge, atiphe, natipulule. Koma tikadagulitsidwa tikhale akapolo ndi adzakazi, ndikadakhala chete; chinkana wosautsa sakadakhoza kubwezera kusowa kwa mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa kuti atiwononge, atiphe ndi kutifafaniziratu. Akanangotigulitsa kokha tikanakhala chete, chifukwa chimene mdani wathuyo akanakupatsani mfumu sibwenzi mutasowa nacho mtendere.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti tagulitsidwa; ine ndi anthu amtundu wanga, kuti ationonge, atiphe, natipulule, Koma tikadagulitsidwa tikhale akapolo ndi adzakazi, ndikadakhala cete; cinkana wosautsa sakadakhoza kubwezera kusowa kwa mfumu.