Esther 7:5 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu Ahasuwero inalankhula, niti kwa mkazi wamkulu Estere, Ndani uyu, ali kuti iyeyu wadzazidwa mtima wake kuti azitero?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Ahasiwero anamufunsa mfumukazi Estere, “Kodi iyeyu ndi ndani ndipo ali kuti amene saopa kuchita chinthu chotere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu Ahaswero inalankhula, niti kwa mkazi wamkuru Estere, Ndani uyu, ali kuti iyeyu wadzazidwa mtima wace kuti azitero?