Esther 8:10 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analembera m'dzina la mfumu Ahasuwero, nasindikiza ndi mphete ya mfumu, natumiza akalata ndi amtokoma pa akavalo, okwera pa akavalo aliwiro achifumu, obadwa mosankhika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mordekai analemba makalatawo mʼdzina la mfumu Ahasiwero, nawadinda ndi chizindikiro cha mphete ya mfumu. Ndipo anawatumiza ndi anthu amithenga amene anakwera pa akavalo a ufumu othamanga kwambiri obadwa mu khola la ufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analembera m'dzina la mfumu Ahaswero, nasindikiza ndi mphete ya mfumu, natumiza akalata ndi amtokoma pa akavalo, okwera pa akavalo aliwiro acifumu, obadwa mosankhika;