Esther 8:14 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natuluka amtokoma okwera pa akavalo aliwiro achifumu; pakuti mau a mfumu anawafulumiza ndi kuwaumiriza; ndipo lamulolo linabukitsidwa m'chinyumba cha ku Susa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atawalamulira a mfumu, amithenga aja anapita nawo makalata mwachangu, atakwera pa akavalo a mfumu. Ndipo lamulolo analiperekanso ku likulu la mzinda wa Susa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naturuka amtokoma okwera pa akavalo aliwiro acifumu; pakuti mau a mfumu anawafulumiza ndi kuwaumiriza; ndipo lamulolo linabukitsidwa m'cinyumba ca ku Susani.