Esther 8:16 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ayuda anali nako kuunika, ndi kukondwera, ndi chimwemwe, ndi ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Ayuda inali nthawi ya nkhope zowala ndi za chimwemwe, chikondwerero ndi ulemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ayuda anali nako kuunika, ndi kukondwera, ndi cimwemwe, ndi ulemu.