Esther 9:10 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ana amuna khumi a Hamani mwana wa Hamedata, mdani wa Ayuda. Koma sanalande zofunkha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ana khumi a Hamani, mwana wa Hamedata, mdani wa Ayuda. Koma sanalande katundu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ana amuna khumi a Hamani mwana wa Hamedata, mdani wa Ayuda. Koma sanalanda zofunkha.