Esther 9:11 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lomwelo anabwera nacho kwa mfumu chiwerengo cha iwo ophedwa m'chinyumba cha ku Susa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lomwelo anawuza mfumu chiwerengero cha anthu amene anaphedwa mu likulu la mzinda wa Susa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lomwelo anabwera naco kwa mfumu ciwerengo ca iwo ophedwa m'cinyumba ca ku Susani.