Esther 9:13 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Estere, Chikakomera mfumu, alole Ayuda okhala m'Susa achite ndi mawa lomwe monga mwa lamulo la lero; ndi ana amuna khumi a Hamani apachikidwe pamtengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Estere anayankha kuti, “Ngati chingakukomereni mfumu, apatseni chilolezo Ayuda okhala mu Susa kuti achitenso zimene achita lerozi mawa, potsata lamulo ndipo mulole kuti ana khumi a Hamani aja mitembo yawo ipachikidwe pa mtanda.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Estere, Cikakomera mfumu, alole Ayuda okhala m'Susani acite ndi mawa lomwe monga mwa lamulo la lero; ndi ana amuna khumi a Hamani apacikidwe pamtengo.