Esther 9:14 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu inati azichita motero, nalamulira m'Susa, napachikidwa ana amuna khumi a Hamani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mfumu inalamula kuti izi zichitike. Anapereka lamulo mu Susa ndipo mitembo ya ana khumi a Hamani anayipachika pa mtanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu inati azicita motero, nalamulira m'Susani, napacikidwa ana amuna khumi a Hamani.