Esther 9:15 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ayuda okhala m'Susa anasonkhana pamodzi, tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi wa Adara, napha amuna mazana atatu m'Susa; koma sanalande zofunkha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ayuda a mu mzinda wa Susa anasonkhana pamodzi pa tsiku la 14 la mwezi wa Adara ndipo anapha anthu 300 mu Susa, koma sanatenge katundu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ayuda okhala m'Susani anasonkhana pamodzi, tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi wa Adara, napha amuna mazana atatu m'Susani; koma sanalanda zofunkha.