Esther 9:20 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mordekai analembera izi, natumiza akalata kwa Ayuda onse okhala m'maiko onse a mfumu Ahasuwero, a kufupi ndi a kutali,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mordekai analemba mawu awa mʼmakalata ndipo anawatumiza kwa Ayuda onse okhala mʼzigawo zonse za mfumu Ahasiwero, a pafupi ndi a kutali:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Moredekai analembera izi, natumiza akalata kwa Ayuda onse okhala m'maiko onse a mfumu Ahaswero, a kufupi ndi a kutali,