Esther 9:21 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuwalimbikitsira, asunge tsiku lakhumi ndi chinai, mwezi wa Adara, ndi tsiku lake lakhumi ndi chisanu lomwe, chaka ndi chaka,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anati chaka chilichonse, Ayudawo azisunga tsiku la 14 ndi 15 la mwezi wa Adara,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuwalimbikitsira, asunge tsiku lakhumi ndi cinai, mwezi wa Adara, ndi tsiku lace lakhumi ndi cisanu lomwe, caka ndi caka,