Esther 9:23 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ayuda anavomereza kuchita monga umo adayambira, ndi umo Mordekai adawalembera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Ayuda anavomereza kusunga masikuwa ngati a chikondwerero monga analembera Mordekai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ayuda anabvomereza kucita monga umo adayambira, ndi umo Moredekai adawalembera;