Esther 9:25 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma pofika mlanduwo kwa mfumu, anati mwa akalata kuti chiwembu chake choipa adachipangira Ayuda, chimbwerere mwini; ndi kuti iye ndi ana amuna ake apachikidwe pamtengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mfumu itazindikira za chiwembuchi, inalamula kuti zilembedwe mʼmakalata kuti chiwembu chimene Hamani anakonzera Ayuda chigwere pa iye mwini, ndi kuti iye pamodzi ndi ana ake apachikidwe pa mtanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma pofika mlanduwo kwa mfumu, anati mwa akalata kuti ciwembu cace coipa adacipangira Ayuda, cimbwerere mwini; ndi kuti Iye ndi ana amuna ace apacikidwe pamtengo,