Esther 9:26 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anatcha masikuwa Purimu, ndilo dzina la ulawo. Momwemo, chifukwa cha mau onse a kalatayo, ndi izi adaziona za mlanduwo, ndi ichi chidawadzera,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi chifukwa chake masiku amenewa amatchedwa masiku a Purimu potsata dzina lakuti Purimu. Chifukwa cha kalata ya Mordekai ndiponso chifukwa cha zimene anaziona ndi kuwachitikira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anacha masikuwa Purimu, ndilo dzina la ulawo. Momwemo, cifukwa ca mau onse a kalatayo, ndi izi adaziona za mlanduwo, ndi ici cidawadzera,