Esther 9:30 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natumiza iye akalata kwa Ayuda onse, kumaiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri a ufumu wa Ahasuwero, ndiwo mau a mtendere ndi choonadi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mordekai anatumiza makalata kwa Ayuda onse ku zigawo 127 za ufumu wa Ahasiwero. Kalatayi inali ya mawu a mtendere ndiponso a kukhulupirika
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natumiza iye akalata kwa Ayuda onse, ku maiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri a ufumu wa Ahaswero, ndiwo mau a mtendere ndi coonadi;