Esther 9:4 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mordekai anali wamkulu m'nyumba ya mfumu, ndi mbiri yake idabuka m'maiko onse; pakuti munthuyu Mordekai anakulakulabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pajatu Mordekai anali munthu wamkulu mʼnyumba ya ufumu. Mbiri yake inafalikira zigawo zonse, ndipo mphamvu zake zinakulirakulirabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Moredekai anali wamkuru m'nyumba ya mfumu, ndi mbiri yace idabuka m'maiko onse; pa kuti munthuyu Moredekai anakula-kulabe.